Eksodo 14:20 BL92

20 nulowa pakati pa ulendo wa Aaigupto ndi ulendo wa Aisrayeli ndipo mtambo unacita mdima, komanso unaunikira usiku; ndipo ulendo wina sunayandikizana ndi unzace usiku wonse.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 14

Onani Eksodo 14:20 nkhani