Eksodo 14:22 BL92

22 Ndipo ana a Israyeli analowa pakati pa nyanja pouma; ndi madziwo anakhala kwa iwo ngati khoma palamanja, ndi palamanzere.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 14

Onani Eksodo 14:22 nkhani