31 Ndipo Israyeli anaiona nchito yaikuru imene Yehova anacitira Aaigupto, ndipo anthuwo anaopa Yehova; nakhulupirira Yehova ndi mtumiki wace Mose.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 14
Onani Eksodo 14:31 nkhani