13 Mwa cifundo canu mwatsogolera anthu amene mudawaombola;Mwa mphamvu yanu mudawalondolera njira yakumka pokhala panu poyera.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 15
Onani Eksodo 15:13 nkhani