Eksodo 15:9 BL92

9 Mdani anati,Ndiwalondola, ndiwakumika, ndidzagawa zofunkha;Ndidzakhuta nao mtima;Ndidzasolola lupanga langa, dzanja langa lidzawaononga.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 15

Onani Eksodo 15:9 nkhani