20 Koma sanammvera Mose; ndipo ena anasiyako kufikira m'mawa; koma unagwa mphutsi, nununkha. Ndipo Mose anakwiya nao.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 16
Onani Eksodo 16:20 nkhani