Eksodo 16:31 BL92

31 Ndipo mbumba ya Israyeli inaucha dzina lace Mana; ndiwo ngati zipatso zampasa, oyera; powalawa akunga timitanda tosanganiza ndi uci.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 16

Onani Eksodo 16:31 nkhani