33 Ndipo Mose anati kwa Aroni, Tenga mphika, nuthiremo mana odzala omeri, nuuike pamaso pa Yehova, usungikire mibadwo yanu.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 16
Onani Eksodo 16:33 nkhani