6 Ndipo Mose ndi Aroni ananena ndi ana onse a Israyeli, Madzulo mudzadziwa kuti Yehova anakuturutsani m'dziko la Aigupto;
Werengani mutu wathunthu Eksodo 16
Onani Eksodo 16:6 nkhani