Eksodo 17:2 BL92

2 Pamenepo anthu anatsutsana ndi Mose, nati, Tipatseni madzi timwe, Koma Mose ananena nao, Mutsutsana nane bwanji? Muyeseranji Yehova?

Werengani mutu wathunthu Eksodo 17

Onani Eksodo 17:2 nkhani