10 Nati Yetero, Woyamikika Yehova, amene anakulanditsani m'dzanja la Aaigupto, ndi m'dzanja la Farao; ameneanalanditsa anthu awa pansi pa dzanja la Aaigupto.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 18
Onani Eksodo 18:10 nkhani