Eksodo 18:2 BL92

2 Ndipo Yetero, mpongozi wa Mose, anabwera naye Zipora mkazi wa Mose (atamtuma kwao), ndi ana ace awiri;

Werengani mutu wathunthu Eksodo 18

Onani Eksodo 18:2 nkhani