Eksodo 19:12 BL92

12 Ndipo ukalembere anthu malire pozungulira, ndi kuti, Muzicenjera musakwere m'phiri, musakhudza cilekezero cace; wokhudza phirilo adzaphedwa ndithu;

Werengani mutu wathunthu Eksodo 19

Onani Eksodo 19:12 nkhani