Eksodo 20:12 BL92

12 Uzilemekeza atate wako ndi amako; kuti acuruke masiku ako m'dziko limene Yehova Mulungu wako akupatsa iwe.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 20

Onani Eksodo 20:12 nkhani