4 Usadzipangire iwe wekha fano losema, kapena cifaniziro ciri conse ca zinthu za m'thambo la kumwamba, kapena za m'dziko lapansi, kapena za m'madzi a pansi pa dziko;
Werengani mutu wathunthu Eksodo 20
Onani Eksodo 20:4 nkhani