7 Usaehule dzina la Yehova Mulungu wako pacabe; cifukwa Yehova sadzamuyesa iye wosacimwa, amene achula pacabe dzina lacelo.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 20
Onani Eksodo 20:7 nkhani