Eksodo 21:14 BL92

14 Koma munthu akacita dala pa mnzace, kumupha monyenga; uzimcotsa ku guwa langa la nsembe, kuti afe.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 21

Onani Eksodo 21:14 nkhani