Eksodo 21:16 BL92

16 Iye wakuba munthu, angakhale wamgulitsa, kapena akampeza m'dzanja lace, aphedwe ndithu.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 21

Onani Eksodo 21:16 nkhani