Eksodo 21:32 BL92

32 Ng'ombeyo ikatunga mnyamata kapena mdzakazi, azipatsa mbuye wace ndalama za masekele a siliva makumi atatu, ndipo ng'ombeyo aiponye miyala.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 21

Onani Eksodo 21:32 nkhani