35 Ng'ombe ya mwini ikapweteka ng'ombe ya mnzace, nifa, azigulitsa ng'ombe yamoyoyo, nagawe ndalama zace; naigawe, ndi yakufa yomweyo.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 21
Onani Eksodo 21:35 nkhani