6 pamenepo mbuye wace azifika naye kwa oweruza, nafike naye kukhomo, kapena kumphuthu, ndipo mbuye wace amboole khutu lace ndi lisungulu; ndipo iye azimgwirira nchito masiku onse.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 21
Onani Eksodo 21:6 nkhani