Eksodo 21:8 BL92

8 Akapanda kumkonda mbuye wace, amene anamtoma mwini yekha, azilola kuti amuombole; alibe mphamvu yakumgulitsa kwa anthu acilendo, popeza wacita naye monyenga.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 21

Onani Eksodo 21:8 nkhani