6 Ukayaka moto, nukalandira kuminga, kotero kuti unyeketsa mulu wa tirigu, kapena tirigu wosasenga, kapena munda; woyatsa motoyo alipe ndithu.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 22
Onani Eksodo 22:6 nkhani