16 ndi madyerero a masika, zipatso zoyamba za nchito zako, zimene udazibzala m'munda; ndi madyerero a kututa, pakutha caka, pamene ututa nchito zako za m'munda.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 23
Onani Eksodo 23:16 nkhani