14 Ndipo anati kwa akuru, Tilindeni kuno kufikira tidzabwera kwa inu; ndipo taonani, Aroni ndi Huri ali nanu; munthu akakhala ndi mlandu abwere kwa iwowa.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 24
Onani Eksodo 24:14 nkhani