23 Ndipo uzipanga gome la mtengo wasitimu; utali wace mikono iwiri, ndi kupingasa kwace mkono umodzi, ow msinkhu wace mkono ndi hafu.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 25
Onani Eksodo 25:23 nkhani