Eksodo 25:26 BL92

26 Nulipangire mphete zinai zagolidi, ndi kuika mphetezo pa ngondya zinai zokhala pa miyendo yace inai.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 25

Onani Eksodo 25:26 nkhani