Eksodo 25:29 BL92

29 Ndipo uzipanga mbale zace, ndi zipande zace, ndi mitsuko yace, ndi zikho zace zakuthira nazo; uzipanga za golidi woona.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 25

Onani Eksodo 25:29 nkhani