13 Ndi mkono wa pa mbali yino, ndi mkono wa pa mbali inzace, wakutsalira m'utali wace wa nsaru za hemalo, icinge pambali zace za kacisi, mbali yino ndi mbali yina, kumphimba.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 26
Onani Eksodo 26:13 nkhani