31 Ndipo uziomba nsaru yocinga ya thonje lamadzi, ndi lofiirira ndi lofiira, ndi la bafuta wa thonje losansitsa, aiombe ndi akerubi nchito ya mmisiri;
Werengani mutu wathunthu Eksodo 26
Onani Eksodo 26:31 nkhani