1 Ndipo upange guwa la nsembe la mtengo wasitimu, utali wace mikono isanu, ndi kupingasa kwace mikono isanu, guwa la nsembelo likhale lampwamphwa, ndi msinkhu wace mikono itatu.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 27
Onani Eksodo 27:1 nkhani