Eksodo 27:14 BL92

14 Ndi nsaru zocingira za pa mbali imodzi ya kucipata zikhale za mikono khumi ndi isanu; nsici zace zikhale zitatu, ndi makamwa ao atatu.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 27

Onani Eksodo 27:14 nkhani