11 Uloce miyala iwiriyo ndi maina a ana a Israyeli, monga mwa nchito ya woloca miyala, monga malembedwe a cosindikizira, uipange igwirike ndi zoikamo zagolidi,
Werengani mutu wathunthu Eksodo 28
Onani Eksodo 28:11 nkhani