25 Koma nsonga zace ziwiri za maunyolo opotawo uzimange ku zoikamo ziwiri, ndi kuziika pa zapamapewa ziwiri za efodi, m'tsogolo mwace.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 28
Onani Eksodo 28:25 nkhani