Eksodo 29:30 BL92

30 mwana wace wamwamuna amene adzakhala wansembe m'malo mwace azibvala masiku asanu ndi awiri, pakulowa iye m'cihema cokomanako kutumikira m'malo opatulika.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 29

Onani Eksodo 29:30 nkhani