Eksodo 29:32 BL92

32 Ndipo Aroni ndi ana ace amuna adye nyama ya nkhosa yamphongoyo, ndi mkate uli mumtanga, pa khomo la cihema cokomanako.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 29

Onani Eksodo 29:32 nkhani