35 Ndipo utero nao Aroni, ndi ana ace amuna, monga mwa zonse ndakuuza; udzaze manja ao masiku asanu ndi awiri.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 29
Onani Eksodo 29:35 nkhani