46 Ndipo adzadziwa kuti Ine ndine Yehova Mulungu wao, amene ndinawaturutsa m'dziko la Aigupto, kuti ndikhale pakati pao. Ine ndine Yehova Mulungu wao.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 29
Onani Eksodo 29:46 nkhani