15 Agwire nchito masiku asanu ndi limodzi; koma lacisanu ndi ciwiri ndilo Sabata lakupumula, lopatulika la Yehova; ali yense wogwira nchito tsiku la Sabata aphedwe ndithu.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 31
Onani Eksodo 31:15 nkhani