18 Koma iye anati, Phokosoli sindilo la kupfuula kwa olakika, kapena la kupfuula kwa opasuka; koma phokoso ndikumvali ndilo la othirirana mang'ombe.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 32
Onani Eksodo 32:18 nkhani