Eksodo 32:26 BL92

26 Mose anaima pa cipata ca cigono, nati, Onse akubvomereza Yehova, adze kwa ine. Pamenepo ana amuna onse a Levi anasonkhana kwa iye,

Werengani mutu wathunthu Eksodo 32

Onani Eksodo 32:26 nkhani