34 Ndipo tsopano, muka, tsogolera anthu kumka nao kumene ndinakuuza; taona, mthenga wanga akutsogolera; koma tsiku lakuwazonda Ine ndidzawalanga cifukwa ca kucimwa kwao.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 32
Onani Eksodo 32:34 nkhani