Eksodo 33:17 BL92

17 Ndipo Yehova anati kwa Mose, Ici comwe wanenaci ndidzacita; pakuti wapeza ufulu pamaso panga, ndipo ndikudziwa dzina lako.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 33

Onani Eksodo 33:17 nkhani