28 Ndipo anakhala pomwepo ndi Yehova masiku makumi anai, usana ndi usiku; sanadya mkate kapena kumwa madzi. Ndipo analembera pa magomewo mau a panganolo, mau khumiwo.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 34
Onani Eksodo 34:28 nkhani