3 Palibe munthu akwere ndi iwe, asaonekenso munthu ali yense m'phiri monse; ndi zoweta zazing'ono kapena zoweta zazikuru zisadye kuphiri kuno.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 34
Onani Eksodo 34:3 nkhani