16 Ndipo anamanga pamodzi nsaru zisanu pa zokha, ndi nsaru zisanu ndi imodzi pa zokha.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 36
Onani Eksodo 36:16 nkhani