Eksodo 36:2 BL92

2 Ndipo Mose adaitana Bezaleli ndi Aholiabu, ndi anthu onse aluso, amene Yehova adaika luso m'mtima mwao, onse ofulumidwa mtima ayandikize kunchito kuicita.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 36

Onani Eksodo 36:2 nkhani