35 Ndipo anaomba nsaru yocinga ndi lamadzi, ndi lofiirira, ndi lofiira, ndi bafuta wa thonje losansitsa; anaciomba ndi akerubi nchito ya mmisiri.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 36
Onani Eksodo 36:35 nkhani