37 Ndipo anaomba nsaru yotsekera pa khomo la cihemaco, ya lamadzi, ndi lofiirira, ndi lofiira, ndi bafuta wa thonje losansitsa, nchito ya wopikula;
Werengani mutu wathunthu Eksodo 36
Onani Eksodo 36:37 nkhani