26 Ndipo analikuta ndi golidi woona, pamwamba pace, ndi mbali zace pozungulira, ndi nyanga zace; ndipo analipangira mkombero wagolidi pozungulira pace.
Werengani mutu wathunthu Eksodo 37
Onani Eksodo 37:26 nkhani